Masalimo 19:2 - Buku Lopatulika Usana ndi usana uchulukitsa mau, ndipo usiku ndi usiku uonetsa nzeru. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Usana ndi usana uchulukitsa mau, ndipo usiku ndi usiku uonetsa nzeru. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Usana umasimbira zimenezo usana unzake, usiku umadziŵitsa zimenezo usiku unzake. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Tsiku ndi tsiku zimayankhula mawu ambiri, usiku ndi usiku zimaonetsa poyera nzeru. |
Ndipo Mulungu anapanga thambo, nalekanitsa madzi anali pansi pathambolo ndi madzi anali pamwamba pathambolo; ndipo kunatero.
Pakukhalabe masiku a dziko lapansi, nthawi yakubzala ndi yakukunkha, chisanu ndi mafundi, malimwe ndi msakasa, usana ndi usiku sizidzalekai.
Wamoyo, wamoyo, iye adzakuyamikani inu, monga ine lero; Atate adzadziwitsa ana ake zoona zanu.