Masalimo 74:16 - Buku Lopatulika16 Usana ndi wanu, usikunso ndi wanu, munakonza kuunika ndi dzuwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Usana ndi wanu, usikunso ndi wanu, munakonza kuunika ndi dzuwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Mudalenga usana ndi usiku. Mudaika mwezi ndi dzuŵa m'malo mwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Masana ndi anu ndipo usiku ndi wanunso; Inuyo munakhazikitsa dzuwa ndi mwezi. Onani mutuwo |