Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 74:17 - Buku Lopatulika

17 Munaika malekezero onse a dziko lapansi; munalenga dzinja ndi malimwe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Munaika malekezero onse a dziko lapansi; munalenga dzinja ndi malimwe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Mudalemba malire a dziko lapansi, mudakhazikitsa chilimwe ndi dzinja.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Ndinu amene munakhazikitsa malire onse a dziko lapansi; munakhazikitsa chilimwe ndi dzinja.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 74:17
6 Mawu Ofanana  

Pakukhalabe masiku a dziko lapansi, nthawi yakubzala ndi yakukunkha, chisanu ndi mafundi, malimwe ndi msakasa, usana ndi usiku sizidzalekai.


Kodi unazindikira chitando cha dziko lapansi? Fotokozera, ngati uchidziwa chonse.


Koma sanadzisiyire Iye mwini wopanda umboni, popeza anachita zabwino, nakupatsani inu zochokera kumwamba mvula ndi nyengo za zipatso, ndi kudzaza mitima yanu ndi chakudya ndi chikondwero.


ndipo ndi mmodzi analenga mitundu yonse ya anthu, kuti akhale ponse pa nkhope ya dziko lapansi, atapangiratu nyengo zao, ndi malekezero a pokhala pao;


Pamene Wam'mwambamwamba anagawira amitundu cholowa chao, pamene anagawa ana a anthu, anaika malire a mitundu ya anthu, monga mwa kuwerenga kwao kwa ana a Israele.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa