Masalimo 74:15 - Buku Lopatulika15 Mudagawa kasupe ndi mtsinje; mudaphwetsa mitsinje yaikulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Mudagawa kasupe ndi mtsinje; mudaphwetsa mitsinje yaikulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Mudatumphutsa akasupe ndi mifuleni, mudaumitsa mitsinje imene siiphwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Ndinu amene munatsekula akasupe ndi mitsinje, munawumitsa mitsinje imene siphwa nthawi zonse. Onani mutuwo |