Masalimo 19:1 - Buku Lopatulika1 Zakumwamba zimalalikira ulemerero wa Mulungu; ndipo thambo lionetsa ntchito ya manja ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Zakumwamba zimalalikira ulemerero wa Mulungu; ndipo thambo lionetsa ntchito ya manja ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Zakumwamba zimalalika ulemerero wa Mulungu, thambo limasonyeza ntchito za manja ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Zakumwamba zimalengeza za ulemerero wa Mulungu; thambo limalalikira ntchito za manja ake. Onani mutuwo |