Masalimo 19:2 - Buku Lopatulika2 Usana ndi usana uchulukitsa mau, ndipo usiku ndi usiku uonetsa nzeru. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Usana ndi usana uchulukitsa mau, ndipo usiku ndi usiku uonetsa nzeru. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Usana umasimbira zimenezo usana unzake, usiku umadziŵitsa zimenezo usiku unzake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Tsiku ndi tsiku zimayankhula mawu ambiri, usiku ndi usiku zimaonetsa poyera nzeru. Onani mutuwo |