Masalimo 19:3 - Buku Lopatulika3 Palibe chilankhulidwe, palibe mau; liu lao silimveka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Palibe chilankhulidwe, palibe mau; liu lao silimveka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Palibe kulankhula, palibe kunena mau aliwonse. Liwu lao silimveka konse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Palibe kuyankhula, palibe mawu aliwonse; liwu lawo silimveka. Onani mutuwo |