Masalimo 19:4 - Buku Lopatulika4 Muyeso wao wapitirira padziko lonse lapansi, ndipo mau ao ku malekezero a m'dziko muli anthu. Iye anaika hema la dzuwa m'menemo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Muyeso wao wapitirira pa dziko lonse lapansi, ndipo mau ao ku malekezero a m'dziko muli anthu. Iye anaika hema la dzuwa m'menemo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Komabe uthenga wao umafalikira pa dziko lonse lapansi. Mau aowo amafika mpaka ku mathero a dziko. Mulungu adamangira dzuŵa nyumba m'thambomo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Koma uthenga wawo umapita pa dziko lonse lapansi, mawuwo amafika mpaka kumalekezero a dziko lapansi. Onani mutuwo |