Masalimo 19:5 - Buku Lopatulika5 ndipo lili ngati mkwati wakutuluka m'chipinda mwake, likondwera ngati chiphona kuthamanga m'njira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 ndipo lili ngati mkwati wakutuluka m'chipinda mwake, likondwera ngati chiphona kuthamanga m'njira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Dzuŵalo limatuluka ngati mkwati wokondwa amene akutuluka m'nyumba mwake, ndipo limayenda ndi chimwemwe ngati ngwazi yamphamvu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Dzuwa lili ngati mkwatibwi wobwera kuchokera ku nsanja yake, ngati katswiri wokondwerera kuthamanga pa mpikisano. Onani mutuwo |