Masalimo 19:6 - Buku Lopatulika6 Kutuluka kwake lituluka kolekezera thambo, ndipo kuzungulira kwake lifikira ku malekezero ake; ndipo kulibe kanthu kobisalira kutentha kwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Kutuluka kwake lituluka kolekezera thambo, ndipo kuzungulira kwake lifikira ku malekezero ake; ndipo kulibe kanthu kobisalira kutentha kwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Limatuluka kuyambira ku mathero ena a thambo, ndi kuzungulira mpaka ku mathero enanso. Palibe chinthu chilichonse chotha kulewa kutentha kwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Limatuluka kuyambira mbali ina ya thambo ndi kuzungulira mpaka mbali inanso; palibe chinthu chotha kupewa kutentha kwake. Onani mutuwo |