Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 148:12 - Buku Lopatulika

12 Anyamata ndiponso anamwali; okalamba pamodzi ndi ana.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Anyamata ndiponso anamwali; okalamba pamodzi ndi ana.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Inu anyamata pamodzi ndi anamwali, inu nkhalamba ndi ana omwe!

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Inu anyamata ndi anamwali, inu nkhalamba ndi ana omwe.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 148:12
7 Mawu Ofanana  

Oimbira anatsogolera, oimba zoimba anatsata m'mbuyo, pakatipo anamwali oimba mangaka.


M'kamwa mwa makanda ndi oyamwa munakhazikitsa mphamvu, chifukwa cha otsutsana ndi Inu, kuti muwaletse mdani ndi wobwezera chilango.


Ndipo namwali adzasangalala m'masewero, ndi anyamata ndi nkhalamba pamodzi; pakuti ndidzasandutsa kulira kwao kukhale kukondwera, ndipo ndidzatonthoza mitima yao, ndi kuwasangalatsa iwo asiye chisoni chao.


Pakuti ukoma wake ndi waukulu ndithu, ndi kukongola kwake nkwakukulu ndithu! Tirigu adzakometsera anyamata, ndi vinyo watsopano anamwali.


Ndipo pakuyandikira Iye tsono potsetsereka pake paphiri la Azitona, unyinji wonse wa ophunzira anayamba kukondwera ndi kuyamika Mulungu ndi mau aakulu, chifukwa cha ntchito zonse zamphamvu anaziona;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa