Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 148:11 - Buku Lopatulika

11 Mafumu a padziko ndi mitundu yonse ya anthu; zinduna ndi oweruza onse a padziko.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Mafumu a padziko ndi mitundu yonse ya anthu; zinduna ndi oweruza onse a padziko.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Inu mafumu a pa dziko lapansi ndi anthu a mitundu yonse, inu akuluakulu ndi olamulira dziko lapansi!

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Inu mafumu a dziko lapansi ndi anthu a mitundu yonse, inu akalonga ndi olamulira a dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 148:11
12 Mawu Ofanana  

Pamenepo amitundu adzaopa dzina la Yehova, ndi mafumu onse a dziko lapansi ulemerero wanu.


Amitundu onse mudawalenga adzadza nadzagwada pamaso panu, Ambuye; nadzalemekeza dzina lanu.


Ndipo mafumu adzakulera, ndi akazi ao aakulu adzakuyamwitsa; iwo adzakugwadira ndi nkhope zao zoyang'ana pansi, nadzaseteka fumbi la m'mapazi ako: ndipo iwe udzadziwa kuti Ine ndine Yehova, ndi iwo amene alindira Ine sadzakhala ndi manyazi.


Ndipo amitundu adzafika kwa kuunika kwako, ndi mafumu kwa kuyera kwa kutuluka kwako.


Ndipo amitundu adzayendayenda mwa kuunika kwake; ndi mafumu a dziko atenga ulemerero wao kulowa nao momwemo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa