Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 148:10 - Buku Lopatulika

10 Nyama zakuthengo ndi zoweta zonse; zokwawa, ndi mbalame zakuuluka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Nyama za kuthengo ndi zoweta zonse; zokwawa, ndi mbalame zakuuluka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Inu nyama zakutchire ndi zoŵeta zonse, inu zinthu zokwaŵa ndi mbalame zouluka!

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 inu nyama zakuthengo ndi ngʼombe zonse, inu zolengedwa zingʼonozingʼono ndi mbalame zowuluka.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 148:10
7 Mawu Ofanana  

iwo, ndi zamoyo zonse monga mwa mitundu yao, ndi zinyama zonse monga mwa mitundu yao, zokwawa zonse zokwawa padziko lapansi monga mwa mitundu yao, ndi zouluka zonse monga mwa mitundu yao, ndi mbalame zonse za mitundumitundu.


Lemekezani Yehova, inu, ntchito zake zonse, ponseponse pali ufumu wake: Lemekeza Yehova, moyo wanga iwe.


Zonse zakupuma zilemekeze Yehova. Aleluya.


Nyama za m'thengo zidzandilimekeza, ankhandwe ndi nthiwatiwa; chifukwa ndipatsa madzi m'chipululu, ndi mitsinje m'mkhwangwala, ndimwetse anthu anga osankhika;


paphiri lothuvuka la Israele ndidzaioka, ndipo idzaphuka nthambi ndi kubala zipatso, nidzakhala mkungudza wokoma, ndi m'munsi mwake mudzakhala mbalame zilizonse za mapiko aliwonse; mu mthunzi wa nthambi zake zidzabindikira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa