Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 148:9 - Buku Lopatulika

9 mapiri ndi zitunda zonse; mitengo yazipatso ndi yamikungudza yonse:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 mapiri ndi zitunda zonse; mitengo yazipatso ndi yamikungudza yonse:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Inu mapiri onse ndi zitunda zonse, inu mitengo yazipatso ndi mikungudza yonse!

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 inu mapiri ndi zitunda zonse, inu mitengo ya zipatso ndi mikungudza yonse,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 148:9
11 Mawu Ofanana  

Chipululu ndi mizinda yake ikweze mau ao, midzi imene Kedara akhalamo; okhala mu Sela aimbe, akuwe kuchokera pamwamba pa mapiri.


Imbani m'mwamba inu, pakuti Yehova wachichita icho; kuwani inu, mbali za pansi padziko; imbani mapiri inu; nkhalango iwe, ndi mitengo yonse m'menemo; chifukwa kuti Yehova wapulumutsa Yakobo, ndipo adzadzilemekezetsa yekha mwa Israele.


Imbani inu, m'mwamba, nukondwere iwe dziko lapansi, imbani inu mapiri, pakuti Yehova watonthoza mtima wa anthu ake, nadzachitira chifundo ovutidwa ake.


Mwenzi mutang'amba kumwamba ndi kutsikira pansi, kuti mapiri agwedezeke pamaso panu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa