Masalimo 71:12 - Buku Lopatulika Musandikhalire kutali, Mulungu; fulumirani kundithandiza, Mulungu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Musandikhalire kutali, Mulungu; fulumirani kundithandiza, Mulungu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Inu Mulungu, musandikhalire kutali. Inu Mulungu wanga, fulumirani kudzandithandiza. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Musakhale kutali ndi ine Inu Mulungu, bwerani msanga, Inu Mulungu wanga; thandizeni. |
Fulumirani ndiyankheni, Yehova; mzimu wanga ukutha. Musandibisire nkhope yanu; ndingafanane nao akutsikira kudzenje.
Koma ine ndine wozunzika ndi waumphawi; mundifulumirire, Mulungu. Inu ndinu mthandizi wanga ndi Mpulumutsi wanga; musachedwe, Yehova.