Masalimo 69:18 - Buku Lopatulika18 Yandikizani moyo wanga, ndi kuuombola; ndipulumutseni chifukwa cha adani anga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Yandikizani moyo wanga, ndi kuuombola; ndipulumutseni chifukwa cha adani anga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Senderani pafupi, mundiwombole, mundipulumutse kwa adani anga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Bwerani pafupi ndi kundilanditsa; ndiwomboleni chifukwa cha adani anga. Onani mutuwo |