Masalimo 69:19 - Buku Lopatulika19 Mudziwa chotonza changa, ndi manyazi anga, ndi chimpepulo changa. Akundisautsa ali pamaso panu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Mudziwa chotonza changa, ndi manyazi anga, ndi chimpepulo changa. Akundisautsa ali pamaso panu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Inu mumadziŵa m'mene anthu amandinyozera, m'mene amandichititsira manyazi ndi kundichotsera ulemu. Adani anga onse mumaŵadziŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Inu mukudziwa momwe ndanyozedwera, kunyozedwa ndi kuchititsidwa manyazi; adani anga onse ali pamaso panu. Onani mutuwo |