Masalimo 22:11 - Buku Lopatulika11 Musandikhalire kutali; pakuti nsautso ili pafupi, pakuti palibe mthandizi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Musandikhalire kutali; pakuti nsautso ili pafupi, pakuti palibe mthandizi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Musandikhalire kutali, pakuti mavuto ali pafupi kundigwera, ndipo palibe wina wondithandiza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Musakhale kutali ndi ine, pakuti mavuto ali pafupi ndipo palibe wina wondipulumutsa. Onani mutuwo |