Masalimo 22:10 - Buku Lopatulika10 Chibadwire ine anandisiyira Inu, kuyambira kwa mai wanga Mulungu wanga ndinu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Chibadwire ine anandisiyira Inu, kuyambira kwa mai wanga Mulungu wanga ndinu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Ndakhala ndikudalira Inu chibadwire changa, Inu mwakhala Mulungu wanga kuyambira pamene mai wanga adandibala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Chibadwire ine ndinaperekedwa kwa Inu; kuchokera mʼmimba mwa amayi anga Inu mwakhala muli Mulungu wanga. Onani mutuwo |