Masalimo 22:9 - Buku Lopatulika9 Pakuti Inu ndinu wondibadwitsa; wondikhulupiritsa pokhala ine pa bere la mai wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pakuti Inu ndinu wondibadwitsa; wondikhulupiritsa pokhala ine pa bere la mai wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Komabe Inu ndinu amene mudalola kuti ndibadwe. Inu ndinu chikhulupiriro changa, mudandilera bwino ndili mwana woyamwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Komabe Inu ndinu amene munandibadwitsa, munanditulutsa mʼmimba mwa amayi anga. Munachititsa kuti ndizikudalirani ngakhale pa nthawi imene ndinkayamwa. Onani mutuwo |