Masalimo 70:5 - Buku Lopatulika5 Koma ine ndine wozunzika ndi waumphawi; mundifulumirire, Mulungu. Inu ndinu mthandizi wanga ndi Mpulumutsi wanga; musachedwe, Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Koma ine ndine wozunzika ndi waumphawi; mundifulumirire, Mulungu. Inu ndinu mthandizi wanga ndi Mpulumutsi wanga; musachedwe, Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Inu Chauta, ine ndine wolefuka ndi wosoŵa, bwerani msanga kwa ine, Inu Mulungu. Inu ndinu mthandizi wanga ndi Mpulumutsi wanga. Inu Mulungu wanga, musachedwe kudzandithandiza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Koma ine ndine wosauka ndi wosowa; bwerani msanga kwa ine Inu Mulungu. Inu ndinu thandizo langa ndi momboli wanga; Inu Yehova musachedwe. Onani mutuwo |