Masalimo 70:4 - Buku Lopatulika4 Asekerere nakondwerere mwa Inu onse akufuna Inu; nanene kosalekeza iwo akukonda chipulumutso chanu, abuke Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Asekerere nakondwerere mwa Inu onse akufuna Inu; nanene kosalekeza iwo akukonda chipulumutso chanu, abuke Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma onse okufunafunani akondwe ndi kusangalala chifukwa cha Inu. Onse okondwerera chipulumutso chanu, azinena kosalekeza kuti, “Chauta ndi wamkulu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Koma onse amene akufunafuna Inu akondwere ndi kusangalala mwa Inu; iwo amene amakonda chipulumutso chanu nthawi zonse anene kuti, “Mulungu akuzike!” Onani mutuwo |