Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 70:3 - Buku Lopatulika

3 Abwerere, kukhale mphotho ya manyazi ao amene akuti, Hede, hede.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Abwerere, kukhale mphotho ya manyazi ao amene akuti, Hede, hede.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Amene amandinyodola kuti, “Ha, Ha,” achoke ndi manyazi poona kuti alephera.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Onse amene akunena kwa ine kuti, “Aha, aha,” abwerere chifukwa cha manyazi awo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 70:3
10 Mawu Ofanana  

Ndipo andiyasamira m'kamwa mwao; nati, Hede, Hede, diso lathu lidachipenya.


Asanene mumtima mwao, Hede, momwemo! Asanene, Tammeza iye.


Apululuke, mobwezera manyazi ao amene anena nane, Hede, hede.


Adani a moyo wanga achite manyazi, nathawe; chotonza ndi chimpepulo zikute ondifunira choipa.


Lilime langa lomwe lidzalankhula za chilungamo chanu tsiku lonse, pakuti ofuna kundichitira choipa achita manyazi, nadodoma.


nunene kwa ana a Amoni, Tamverani mau a Ambuye Yehova, Atero Ambuye Yehova, Popeza unati, Ha! Kunena malo anga opatulika; muja anadetsedwa ndi kunena dziko la Israele; muja linapasuka ndi kunena nyumba ya Yuda; muja adalowa kundende;


Wobadwa ndi munthu iwe, popeza Tiro ananyodola Yerusalemu, ndi kuti, Ha! Wathyoka uwu udali chipata cha mitundu ya anthu; wanditembenukira ine; ndidzakhuta ine, wapasuka uwu;


Atero Ambuye Yehova, Popeza mdani ananena za inu, Ha! Ingakhale misanje yakale ili yathu, cholowa chathu;


(Uyutu tsono anadzitengera kadziko ndi mphotho ya chosalungama; ndipo anagwa chamutu, naphulika pakati, ndi matumbo ake onse anakhuthuka;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa