Masalimo 70:2 - Buku Lopatulika2 Achite manyazi, nadodome amene afuna moyo wanga. Abwezedwe m'mbuyo, napepulidwe amene akonda kundichitira choipa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Achite manyazi, nadodome amene afuna moyo wanga. Abwezedwe m'mbuyo, napepulidwe amene akonda kundichitira choipa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Anthu ofunafuna moyo wanga, muŵachititse manyazi ndi kuŵasokoneza. Amene akhumba kundipweteka, abwezedwe m'mbuyo ndi kunyozedwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iwo amene akufunafuna moyo wanga achititsidwe manyazi ndi kusokonezedwa; onse amene akukhumba chiwonongeko changa abwezedwe mopanda ulemu. Onani mutuwo |