Masalimo 70:1 - Buku Lopatulika1 Fulumirani kundipulumutsa, Mulungu! Fulumirani kundithandiza, Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Fulumirani kundipulumutsa, Mulungu! Fulumirani kundithandiza, Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Inu Mulungu, pulumutseni. Inu Chauta, fulumirani kudzandithandiza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Fulumirani Mulungu kundipulumutsa; Yehova bwerani msanga kudzandithandiza. Onani mutuwo |