Masalimo 71:1 - Buku Lopatulika1 Ndikhulupirira Inu, Yehova. Ndisachite manyazi nthawi zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndikhulupirira Inu, Yehova. Ndisachite manyazi nthawi zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Ine ndimathaŵira kwa Inu Chauta. Musandichititse manyazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mwa Inu Yehova ine ndathawiramo; musalole kuti ndichititsidwe manyazi. Onani mutuwo |