Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 22:19 - Buku Lopatulika

19 Koma Inu, Yehova, musakhale kutali; mphamvu yanga Inu, mufulumire kundithandiza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Koma Inu, Yehova, musakhale kutali; mphamvu yanga Inu, mufulumire kundithandiza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Koma Inu Chauta musakhale kutali. Inu, mphamvu zanga, fulumirani kudzandithandiza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Koma Inu Yehova, musakhale kutali; Inu mphamvu yanga, bwerani msanga kuti mudzandithandize.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 22:19
8 Mawu Ofanana  

Muimiranji patali, Yehova? Mubisaliranji m'nyengo za nsautso?


Ndikukondani, Yehova, mphamvu yanga.


Yehova, adzasekera mfumu mu mphamvu yanu; adzakondwera kwakukulu m'chipulumutso chanu!


Musandikhalire kutali; pakuti nsautso ili pafupi, pakuti palibe mthandizi.


Ndikupemphani, Yehova, ndilanditseni; fulumirani kudzandithandiza, Yehova.


Ndipo ine ndine wozunzika ndi waumphawi; koma Ambuye andikumbukira ine. Inu ndinu mthandizi wanga, ndi Mpulumutsi wanga, musamachedwa, Mulungu wanga.


Koma ine ndine wozunzika ndi waumphawi; mundifulumirire, Mulungu. Inu ndinu mthandizi wanga ndi Mpulumutsi wanga; musachedwe, Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa