Masalimo 22:18 - Buku Lopatulika18 Agawana zovala zanga, nachita maere pa malaya anga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Agawana zovala zanga, nachita maere pa malaya anga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Agaŵana zovala zanga, ndipo achitira malaya anga maere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Iwo agawana zovala zanga pakati pawo ndi kuchita maere pa zovala zangazo. Onani mutuwo |