Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 22:17 - Buku Lopatulika

17 Ndikhoza kuwerenga mafupa anga onse; iwo ayang'ana nandipenyetsetsa ine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ndikhoza kuwerenga mafupa anga onse; iwo ayang'ana nandipenyetsetsa ine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Mafupa anga akuwonekera, koma anthu aja akungondiyang'anitsitsa akukondwera poona kuti ndikuvutika.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Ine nditha kuwerenga mafupa anga onse; anthu amandiyangʼanitsitsa ndi kundidzuma.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 22:17
8 Mawu Ofanana  

Mnofu wake udatha, kuti sungapenyeke; ndi mafupa ake akusaoneka atuluka.


Monga ambiri anazizwa ndi iwe Israele, momwemo nkhope yake yaipitsidwa ndithu, kupambana munthu aliyense, ndi maonekedwe ake kupambana ana a anthu;


nakhala iwo pansi, namdikira kumeneko.


Ndipo unamtsata unyinji waukulu wa anthu, ndi wa akazi amene anadziguguda pachifuwa, namlirira Iye.


Ndipo anthu anaima alikupenya. Ndi akulunso anamlalatira Iye, nanena, Anapulumutsa ena; adzipulumutse yekha ngati iye ndiye Khristu wa Mulungu, wosankhidwa wake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa