Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 22:20 - Buku Lopatulika

20 Landitsani moyo wanga kulupanga; wokondedwa wanga kumphamvu ya galu,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Landitsani moyo wanga kulupanga; wokondedwa wanga kumphamvu ya galu,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Pulumutsani moyo wanga ku lupanga. Landitseni ku mphamvu za mimbulu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Pulumutsani moyo wanga ku lupanga, moyo wanga wopambanawu ku mphamvu ya agalu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 22:20
7 Mawu Ofanana  

Ukani Yehova, Mumtsekereze, mumgwetse, landitsani moyo wanga kwa woipa ndi lupanga lanu;


Ambuye, mudzapenyererabe nthawi yanji? Bwezani moyo wanga kwa zakundiononga zao, wanga wa wokha kwa misona ya mkango.


Achite manyazi nadodome iwo akulondola moyo wanga kuti auononge. Abwerere m'mbuyo, nachite manyazi iwo okondwera kundichitira choipa.


Yandikizani moyo wanga, ndi kuuombola; ndipulumutseni chifukwa cha adani anga.


Yehova Mulungu wanga, ngati ndachita ichi; ngati m'manja anga muli chosalungama;


Achite manyazi, nadodome amene afuna moyo wanga. Abwezedwe m'mbuyo, napepulidwe amene akonda kundichitira choipa.


Galamuka, lupanga, pa mbusa wanga, ndi pa munthu mnzanga wa pamtima, ati Yehova wa makamu; kantha mbusa, ndi nkhosa zidzabalalika; koma ndidzabwezera dzanja langa pa zazing'onozo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa