Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 22:21 - Buku Lopatulika

21 ndipulumutseni m'kamwa mwa mkango; inde mwandiyankha ine ndili pa nyanga za njati.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 ndipulumutseni m'kamwa mwa mkango; inde mwandiyankha ine ndili pa nyanga za njati.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Pulumutseni kukamwa kwa mkango, mulanditse moyo wanga wovutika ku nyanga za njati.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Ndilanditseni mʼkamwa mwa mikango; pulumutseni ku nyanga za njati.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 22:21
12 Mawu Ofanana  

Ambuye, mudzapenyererabe nthawi yanji? Bwezani moyo wanga kwa zakundiononga zao, wanga wa wokha kwa misona ya mkango.


Ndipo njati zidzatsika ndi iwo, ndi ng'ombe zofula ndi zamphongo; ndi dziko laolao lidzanona ndi mafuta.


Mulungu awatulutsa mu Ejipito; mphamvu yake ikunga ya njati.


Masiku onse, pamene ndinali ndi inu mu Kachisi, simunatanse manja anu kundigwira: koma nyengo ino ndi yanu, ndipo ulamuliro wa mdima ndi wanu.


Sindidzalankhulanso zambiri ndi inu, pakuti mkulu wa dziko lapansi adza; ndipo alibe kanthu mwa Ine;


Pamenepo anatola miyala kuti amponye Iye; koma Yesu anabisala, natuluka mu Kachisi.


Pakuti zoonadi anasonkhanidwa m'mzinda muno Herode, ndi Pontio Pilato yemwe pamodzi ndi amitundu ndi anthu a Israele kumchitira choipa Mwana wanu wopatulika Yesu amene munamdzoza;


Woyamba kubadwa wa ng'ombe yake, ulemerero ndi wake; nyanga zake ndizo nyanga zanjati; adzatunga nazo mitundu ya anthu pamodzi, kufikira malekezero a dziko lapansi. Iwo ndiwo zikwi khumi za Efuremu, iwo ndiwo zikwi za Manase.


Koma Ambuye anaima nane nandipatsa mphamvu; kuti mwa ine chilalikiro chimveke konsekonse, ndi amitundu onse amve; ndipo ndinalanditsidwa m'kamwa mwa mkango.


Khalani odzisungira, dikirani; mdani wanu mdierekezi, monga mkango wobuma, ayendayenda ndi kufunafuna wina akamlikwire:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa