Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 22:22 - Buku Lopatulika

22 Ndidzalalikira dzina lanu kwa abale anga, pakati pa msonkhano ndidzakulemekezani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Ndidzalalikira dzina lanu kwa abale anga, pakati pa msonkhano ndidzakulemekezani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Ndidzasimbira abale anga za dzina lanu. Ndidzatamanda dzina lanu pa msonkhano wa anthu anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Ine ndidzalengeza dzina lanu kwa abale anga; ndidzakutamandani mu msonkhano.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 22:22
11 Mawu Ofanana  

Lemekezo langa lidzakhala la Inu mu msonkhano waukulu, zowinda zanga ndidzazichita pamaso pa iwo akumuopa Iye.


Ndidzakuyamikirani mwa anthu, Ambuye, ndidzakuimbirani mwa mitundu.


Ndipo Mfumuyo idzayankha nidzati kwa iwo, Indetu ndinena kwa inu, Chifukwa munachitira ichi mmodzi wa abale anga, ngakhale ang'onong'ono awa, munandichitira ichi Ine.


Pomwepo Yesu ananena kwa iwo, Musaope; pitani, kauzeni abale anga kuti amuke ku Galileya, ndipo adzandiona Ine kumeneko.


Yesu ananena naye, Usandikhudze, pakuti sinditha kukwera kwa Atate; koma pita kwa abale anga, ukati kwa iwo, Ndikwera kunka kwa Atate wanga, ndi Mulungu wanu.


Chifukwa kuti iwo amene Iye anawadziwiratu, iwowa anawalamuliratu afanizidwe ndi chifaniziro cha Mwana wake, kuti Iye akakhale mwana woyamba wa abale ambiri;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa