Masalimo 40:13 - Buku Lopatulika13 Ndikupemphani, Yehova, ndilanditseni; fulumirani kudzandithandiza, Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndikupemphani, Yehova, ndilanditseni; fulumirani kudzandithandiza, Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Inu Chauta, pulumutseni. Inu Chauta, fulumirani kudzandithandiza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Pulumutseni Yehova; Bwerani msanga Yehova kudzandithandiza. Onani mutuwo |