Masalimo 48:3 - Buku Lopatulika Mulungu adziwika m'zinyumba zake ngati msanje. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mulungu adziwika m'zinyumba zake ngati msanje. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mulungu waonetsa kuti ndiye woteteza mzindawo, pakuti Iye amakhala m'kati mwa malinga ake. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mulungu ali mu malinga ake; Iye wadzionetsa yekha kuti ndiye malinga akewo. |
Ndipo pamene Yehova anaona kuti anadzichepetsa, mau a Yehova anadza kwa Semaya, ndi kuti, Anadzichepetsa; sindidzawaononga; koma katsala kanthawi ndipo ndidzawapatsa chipulumutso, wosatsanulira mkwiyo wanga pa Yerusalemu ndi dzanja la Sisake.
Wakongola, bwenzi langa, namwaliwe ngati Tiriza, wokoma ngati Yerusalemu, woopsa ngati nkhondo ndi mbendera.
Onse opita panjira akuombera manja: Atsonya, napukusira mitu yao pa mwana wamkazi wa Yerusalemu, nati, kodi uwu ndi mzinda wotchedwa wokongola, wangwiro, wokondweretsa dziko lonse?