2 Samueli 5:7 - Buku Lopatulika7 Chinkana anatero Davide anathyola linga la Ziyoni, lomwelo ndilo mzinda wa Davide. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Chinkana anatero Davide anathyola linga la Ziyoni, lomwelo ndilo mudzi wa Davide. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Komabe Davide adalanda linga la Ziyoni, ndiye kuti Mzinda wa Davide. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Komabe Davide analanda linga la Ziyoni, limene ndi mzinda wa Davide. Onani mutuwo |