Masalimo 50:2 - Buku Lopatulika2 Mulungu awalira mu Ziyoni, mokongola mwangwiro. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Mulungu awalira m'Ziyoni, mokongola mwangwiro. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mulungu akuŵala atakhala m'Ziyoni, mzinda wake wokongola kotheratu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Kuchokera ku Ziyoni, mokongola kwambiri Mulungu akuwala. Onani mutuwo |