Masalimo 50:3 - Buku Lopatulika3 Adzafika Mulungu wathu, ndipo sadzakhala chete. Moto udzanyeka pankhope pake, ndipo pozungulira pake padzasokosera kwakukulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Adzafika Mulungu wathu, ndipo sadzakhala chete. Moto udzanyeka pankhope pake, ndipo pozungulira pake padzasokosera kwakukulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mulungu wathu akubwera, sakhala chete. Patsogolo pake pali moto wonyeketsa, M'mbali mwake monse muli mkuntho wamphamvu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mulungu wathu akubwera ndipo sadzakhala chete; moto ukunyeketsa patsogolo pake, ndipo pomuzungulira pali mphepo yamkuntho Onani mutuwo |