Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 46:7 - Buku Lopatulika

7 Yehova wa makamu ali ndi ife; Mulungu wa Yakobo ndiye pamsanje pathu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Yehova wa makamu ali ndi ife; Mulungu wa Yakobo ndiye pamsanje pathu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Chauta Wamphamvuzonse ali nafe. Mulungu wa Yakobe ndiye kothaŵira kwathu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Yehova Wamphamvuzonse ali ndi ife, Mulungu wa Yakobo ndi linga lathu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 46:7
9 Mawu Ofanana  

Ndipo taonani, Mulungu ali nafe, wotitsogolera ndi ansembe ake, ndi malipenga oliza nao chokweza, kukulizirani inu chokweza. Ana a Israele inu, musalimbane naye Yehova Mulungu wa makolo anu; pakuti simudzapindula nako.


Aphokoseranji amitundu, nalingiriranji anthu zopanda pake?


Yehova wa makamu ali ndi ife, Mulungu wa Yakobo ndiye pamsanje pathu.


Ndipo Yehova adzakhala msanje kwa iye wokhalira mphanthi. Msanje m'nyengo za nsautso;


Panganani upo, koma udzakhala chabe; nenani mau, koma sadzachitika; pakuti Mulungu ali pamodzi ndi ife.


Chokhachi musamapikisana naye Yehova, musamaopa anthu a m'dzikomo; pakuti ndiwo mkate wathu; mthunzi wao wawachokera, ndipo Yehova ali nafe; musamawaopa.


ndi kuwaphunzitsa, asunge zinthu zonse zimene ndinakulamulani inu; ndipo onani, Ine ndili pamodzi ndi inu masiku onse, kufikira chimaliziro cha nthawi ya pansi pano.


Ndipo tidzatani ndi zinthu izi? Ngati Mulungu ali ndi ife, adzatikaniza ndani?


Ambuye akhale ndi mzimu wako. Chisomo chikhale nanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa