Numeri 26:7 - Buku Lopatulika Iwo ndiwo mabanja a Arubeni; owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi anai mphambu zitatu kudza mazana asanu ndi awiri mphambu makumi atatu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Iwo ndiwo mabanja a Arubeni; owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi anai mphambu zitatu kudza mazana asanu ndi awiri mphambu makumi atatu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ameneŵa, anthu okwanira 43,730, ndiwo anali a m'mabanja a Rubeni, amene adaŵerengedwa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Awa anali mafuko a Rubeni: onse amene anawerengedwa analipo 43,730. |
owerengedwa ao a fuko la Rubeni, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu ndi chimodzi kudza mazana asanu.
Ndi khamu lake, ndi olembedwa ake, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu ndi chimodzi kudza mazana asanu.
Ndipo kunali, utatha mliriwo, Yehova ananena ndi Mose ndi Eleazara mwana wa Aroni wansembe, nati,
Ndipo ana a Perezi ndiwo: Hezironi, ndiye kholo la banja la Ahezironi; Hamuli, ndiye kholo la banja la Ahamuli.