Numeri 2:11 - Buku Lopatulika11 Ndi khamu lake, ndi olembedwa ake, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu ndi chimodzi kudza mazana asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndi khamu lake, ndi olembedwa ake, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu ndi chimodzi kudza mazana asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 ndipo ankhondo ake ngokwanira 45,500. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 46,500. Onani mutuwo |