Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 2:10 - Buku Lopatulika

10 Mbendera ya chigono cha Rubeni ikhale kumwera monga mwa makamu ao; ndipo kalonga wa ana a Rubeni ndiye Elizuri mwana wa Sedeuri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Mbendera ya chigono cha Rubeni ikhale kumwera monga mwa makamu ao; ndipo kalonga wa ana a Rubeni ndiye Elizuri mwana wa Sedeuri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 “Mbali yakumwera kuzikhala mbendera ya zithando za fuko la Rubeni, m'magulumagulu. Mtsogoleri wa fuko la Rubeni ndi Elizuri mwana wa Sedeuri,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Kummwera kudzakhala magulu a msasa wa Rubeni pamene pali mbendera yawo. Mtsogoleri wa gulu la Rubeni ndi Elizuri mwana wa Sedeuri.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 2:10
8 Mawu Ofanana  

Ndipo ana a Rubeni mwana woyamba wa Israele, (pakuti ndiye mwana woyamba; koma popeza anaipsa kama wa atate wake ukulu wake unapatsidwa kwa ana a Yosefe mwana wa Israele, koma m'buku la chibadwidwe asayesedwe monga mwa ukulu wake.


Ndipo maina a amuna amene aime nanu ndi awa: wa Rubeni, Elizuri mwana wa Sedeuri.


Ndi a mbendera ya chigono cha Rubeni, anayenda monga mwa magulu ao; ndipo pa gulu lake anayang'anira Elizuri mwana wa Sedeuri.


Mukalizanso chokweza, a m'zigono za kumwera ayende; alize chokweza pakumuka.


Ndi khamu lake, ndi olembedwa ake, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu ndi chimodzi kudza mazana asanu.


Tsiku lachinai Elizuri, mwana wa Sedeuri, kalonga wa ana a Rubeni:


ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Elizuri mwana wa Sedeuri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa