Numeri 2:9 - Buku Lopatulika9 Owerengedwa onse a chigono cha Yuda ndiwo zikwi makumi khumi mphambu makumi asanu ndi atatu kudza zisanu ndi chimodzi mphambu mazana anai, monga mwa makamu ao. Ndiwo azitsogolera ulendo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Owerengedwa onse a chigono cha Yuda ndiwo zikwi makumi khumi mphambu makumi asanu ndi atatu kudza zisanu ndi chimodzi mphambu mazana anai, monga mwa makamu ao. Ndiwo azitsogolera ulendo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Gulu lonse lathunthu la ku zithando za Yuda, poŵerenga magulu atatu onseŵa, ndi 186,400. Iwowo azikhala patsogolo poyenda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Anthu onse aamuna mʼmisasa ya Yuda, chiwerengero chawo ndi 186,400 monga mwa magulu awo. Iwowo ndiwo aziyamba kusamuka. Onani mutuwo |