Numeri 2:8 - Buku Lopatulika8 Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zisanu ndi ziwiri kudza mazana anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zisanu ndi ziwiri kudza mazana anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 ndipo ankhondo ake ngokwanira 57,400. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 57,400. Onani mutuwo |