Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -

Numeri 2:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Anthu onse aamuna mʼmisasa ya Yuda, chiwerengero chawo ndi 186,400 monga mwa magulu awo. Iwowo ndiwo aziyamba kusamuka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

9 Owerengedwa onse a chigono cha Yuda ndiwo zikwi makumi khumi mphambu makumi asanu ndi atatu kudza zisanu ndi chimodzi mphambu mazana anai, monga mwa makamu ao. Ndiwo azitsogolera ulendo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Owerengedwa onse a chigono cha Yuda ndiwo zikwi makumi khumi mphambu makumi asanu ndi atatu kudza zisanu ndi chimodzi mphambu mazana anai, monga mwa makamu ao. Ndiwo azitsogolera ulendo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Gulu lonse lathunthu la ku zithando za Yuda, poŵerenga magulu atatu onseŵa, ndi 186,400. Iwowo azikhala patsogolo poyenda.

Onani mutuwo Koperani

Numeri 2:9
2 Mawu Ofanana  

Magulu a msasa wa Yuda ndiwo anayamba kunyamuka potsata mbendera yawo. Mtsogoleri wa gulu lawo anali Naasoni mwana wa Aminadabu.

Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 57,400.

Titsatireni:

Zotsatsa

Zotsatsa