Numeri 26:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo ana a Perezi ndiwo: Hezironi, ndiye kholo la banja la Ahezironi; Hamuli, ndiye kholo la banja la Ahamuli. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo ana a Perezi ndiwo: Hezironi, ndiye kholo la banja la Ahezironi; Hamuli, ndiye kholo la banja la Ahamuli. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Tsono ana aamuna a Perezi anali aŵa: Hezironi anali kholo la banja la Ahezironi. Hamuli anali kholo la banja la Ahamuli. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Zidzukulu za Perezi zinali izi: kuchokera mwa Hezironi, fuko la Ahezironi; kuchokera mwa Hamuli, fuko la Ahamuli. Onani mutuwo |