Numeri 26:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo ana a Yuda monga mwa mabanja ao ndiwo: Sela, ndiye kholo la banja la Asela; Perezi, ndiye kholo la banja la Aperezi; Zera, ndiye kholo la banja la Azera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo ana a Yuda monga mwa mabanja ao ndiwo: Sela, ndiye kholo la banja la Asela; Perezi, ndiye kholo la banja la Aperezi; Zera, ndiye kholo la banja la Azera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Potsata mabanja ao ana ena aamuna a Yuda anali aŵa: Sela anali kholo la banja la Asela. Perezi anali kholo la banja la Aperezi. Zera anali kholo la Azera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Zidzukulu za Yuda monga mwa mafuko awo zinali izi: kuchokera mwa Sela, fuko la Asera; kuchokera mwa Perezi, fuko la Aperezi; kuchokera mwa Zera, mbumba ya Zera. Onani mutuwo |