Numeri 26:19 - Buku Lopatulika19 Ana aamuna a Yuda, ndiwo Eri ndi Onani; ndipo Eri ndi Onani anamwalira m'dziko la Kanani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ana amuna a Yuda, ndiwo Eri ndi Onani; ndipo Eri ndi Onani anamwalira m'dziko la Kanani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Ana aamuna a Yuda anali Ere ndi Onani, koma iwowo adafera m'dziko la Kanani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Eri ndi Onani anali ana aamuna a Yuda, koma anafera mu Kanaani. Onani mutuwo |