Numeri 26:18 - Buku Lopatulika18 Iwo ndiwo mabanja a ana a Gadi, monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi anai ndi mazana asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Iwo ndiwo mabanja a ana a Gadi, monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi anai ndi mazana asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Ameneŵa, anthu okwanira 40,500, ndiwo anali a m'mabanja a Gadi, amene adaŵerengedwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Awa ndiwo anali mafuko a Gadi. Onse amene anawerengedwa analipo 40,500. Onani mutuwo |