Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 26:18 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Awa ndiwo anali mafuko a Gadi. Onse amene anawerengedwa analipo 40,500.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

18 Iwo ndiwo mabanja a ana a Gadi, monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi anai ndi mazana asanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Iwo ndiwo mabanja a ana a Gadi, monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi anai ndi mazana asanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Ameneŵa, anthu okwanira 40,500, ndiwo anali a m'mabanja a Gadi, amene adaŵerengedwa.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 26:18
3 Mawu Ofanana  

kuchokera mwa Arodi, fuko la Aarodi; kuchokera mwa Arieli, fuko la a Areli.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa