Numeri 26:22 - Buku Lopatulika22 Iwo ndiwo mabanja a Yuda monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi asanu ndi awiri mphambu zisanu ndi chimodzi kudza mazana asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Iwo ndiwo mabanja a Yuda monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi asanu ndi awiri mphambu zisanu ndi chimodzi kudza mazana asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Ameneŵa, anthu okwanira 76,500, ndiwo anali a m'mabanja a Yuda, amene adaŵerengedwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Awa ndiwo anali mafuko a Yuda. Amene anawerenga analipo 76,500. Onani mutuwo |